Posts

Showing posts with the label poem

Ndakatulo youkira

IMFA Usachite matama imfa Thakati ndiwe Opanda chisoni Polodza akulu Ndiwedi mbanda Mantha ulibe Wamayi moyo pokhwathula Yosamva mankhwala Nthenda ndiwe kuli chete ana watengera Kwanthawi ndakusaka Ndikakupeza ndikupha Usachite matama imfa.